Ndimalota ndli, ndili mu ndege Nditavala icing ngati keke Ndiye ndikuphusha, mpaka zitheke Timavala Nike sungatithethe, aye Mpakana basi titenthe eh Kutulutsa ina mpaka tibebe eh Scale kukwela mpaka tilemele Kuyesa paliponse ndiye ukazationa tikunjoya Ndi ma kitikiti ih Timayatsa ndi ma pin pin ih Dola yathu siyambiri mbiri ih Koma mbuye ali nafe Ali likiliki ih, aye Izizi, sitipanga mwa Chinsinsi, eish Izizi, timagaya ngati minsi izi, aye Izizi timadyela ngati fees Izizi timadropa ngati leak Pena kuzi kayikila koma Og Anandiuza Phuma nje eh Ndiwe shasha usazaphwekese Kumakhala ndi patience ngati Sheshe One step at a time, ndiye ndimaponya chi stepe Ngati ka jibidi Daily ngati ma pilisi Ku worker mpaka friday ngati ku nzikiti Ndiye musamandiyabwe inuyo nsikidzi Kuzisaka Ngati thumba kuzisaka ah Focused on the goal kuti waka ah Kuthela ma penalty ndiye mukazationa tikuballer Ndi ma kitikiti ih Timayatsa ndi ma pin pin ih Dola yathu siyambiri mbiri ih Koma mbuye ali nafe Ali likiliki ih, aye Izizi, sitipanga mwa Chinsinsi, eish Izizi, timagaya ngati minsi izi (Ndi ma kiti kiti ih, ndi ma pin pin ih) (Siya ya mbili mbili ih, Koma mbuye alinafe ali likiliki ih)