Kishore Kumar Hits

Cozizwa - Miyala текст песни

Исполнитель: Cozizwa

альбом: Miyala


Hey
Hey Heeeyah aye
Heeeyah aye
Pakamwa pomwe ndiimbira nyimbo yanga
Tsiku lina ndithu yahwe adzandifunsa (Funsa funsa funsa)
Pakamwa n'nakupatsa
N'chifukwa chani unkaphyozera zingombingo?
Miyendo yomwe uvinira nyimbo yangayi
Tsiku lina ndithu Yahwe adzakufunsa (Funsa funsa funsa)
Miyendo nnakupatsa
Ona unkapalasila kokabera anthu?
Koma ine, koma ine
Ine ndinsembe yamatamando
Koma ine, koma ine
Ine ndinsembe yamatamando
Musandiuze ndikhale phee
Apo bii Miyala isokosa (Miyala isokosa)
Eeeeh sindikhala phee
Apo bii Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Ndikuti shaa Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Isokosa pano (Miyala isokosa)
Ndikuti eeh Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Isokosa pano (Miyala isokosa)
Ndikuti shaa Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Ilalata pano (Miyala ilalata)
Ndikuti woh Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Heey
Kuli achina mbuzi
Kuli achina ng'ombe
Kuli achina makoswe
Kuli achina mbalame
Kuli achina mphaka
Kuli achina agalu
Kuli achina ntchentche
Kuli achina ngumbi
Ine ndimachita chidwi ndi mwala
Poti mwala ulibe pakamwa
Koma kudzaiyang'ana mbuzi, ili kukamwa yasa
Koma nkadzamuyang'ana galu, naye alikukamwa yasa (Eeeh)
Kudzaiyang'ana mbewa, nayo ili kukamwa yasamuleni
Koma ngati mau akunena, mwala udzaimba nyimbo kuli bwanji makoswe
Ngati mau akunena, mwala udzaimba nyimbo kuli bwanji mbewa
Musandiuze ndikhale phee
Inu apo bii Miyala isokosa (Miyala isokosa)
Eeeeh ndati sindikhala phee
Apo bii Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Ndikuti woh Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Ndikuti woh Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Miyala isokosa pano (Miyala isokosa)
Ndikuti shaa Miyala iyankhula pano
Miyala iyankhula pano
Ehhh Miyala ichezapo pano
Miyala ichezapo pano
Ndikuti woh Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Miyala ilalata pano (Miyala ilalata)
Kuli achina mbewa
Kuli achina nkhuku
Kuli achina mphemvu
Kuli achina gwafa
Kuli achina mbatata
Kuli achina khoswe
Kuli achina nkhuku
Eh ine ndimtama tsiku lonse
Ndimtama tsiku lonse ineyo
Ndati ndimtama tsiku lonse
Ine ndimtama tsiku lonse
Ndimtama tsiku lonse
Ndimtama tsiku lonse
Eeeeh ndati ndimtama tsiku lonse
Ine ndimtama tsiku lonse

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Lawi

Исполнитель

Dali

Исполнитель

Liwu

Исполнитель