Mmmh aah Uh uh Uh uh Mama Saint Realest Monga momwe adamulengera Adamu ndi Hava Ndi momwe tilili Tadikira kupilira kudutsamo mu zokhoma Kwa nthawi yayitali Pano ndikuona maso mphenya Iwe ndi ine takalambitsana Tili ndi ana, ana athu ali ndi ana awo Ngati mwamuna, atasiya makolo ache Wautali, kukakhala ndi mkazi wake Nayeso mkazi, atasiya makolo ache Wautali kukakhala ndi mwamuna wache Tsono tikudikiranji?, iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo momanga banja Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo movekana mphete Ine i can't wait Kuti nzakutengele kunyumba kwa amayi ukawonekele I can't wait Kuti amayi ako ndi amayi anga adzakhale a sewele I can't wait Zija zomagonerana pamwendo, tinkhani tikukambilana Zija zomathamangitsana m'nyumba Kusowetsa mtendere aneba, (i can't wait) Zija zomayambana, mawa mkugwilizana, (i can't wait) Zija zoti lero kutaya chakudya mawa mkugona ndi njala I can't wait kuti udzakhale mayi achiyembekezo Uzadutse muzonse mayi amadutsamo Mwamuna, atasiya makolo ache, (oh Lord) Wautali, kukakhala ndi mkazi wake, (ooh Lord) Nayeso mkazi, atasiya makolo ache Wautali kukakhala ndi mwamuna wache Tsono tikudikiranji?, iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo momanga banja Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo movekana mphete Will you marry me? Will you marry me? Mmh babe I wanna make you be my wife I wanna make you be my wife I wanna make you be my wife! Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo momanga banja Tikudikira! iwe ndi ine Tikudikira! iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo movekana mphete Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine M'malo momanga banja Tikudikiranji? iwe ndi ine Tikudikiranji? iwe ndi ine Ooh! iwe ndi ine Oh babe uh Saint Realest you know