Mathumela Music Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Mphini yobwereza ati imawala asisi Ine sinditopa mpakana umve Nkhani ya dama, sisi mudzayipeza mtsogolo Muphunzire kaye ifeyo tikudalira Kodi maloto akhale kudzakwatiwa ngwachuma? Nanga akadzakusasa chemwali mudzagwira pati? Poti uli ndi mwana isayese dziko latha chemwa Bwerera ku sukulu zinazo zingadikire poti tikudalira iwe Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndamva unong'ona kuti natenga kale matenda Mchemwali wanga simathero a zonse, ih Sitikusiya ndiwe mchemwali wathu Usachewuke mbuyo, tsogolo ndi lowala Tidzidyera limodzi, kugona m'nyumba momo, yeah, yeah Dziwa kupitiliza nkugona ndi amuna Umangodzilakwira, amangowonjezela matenda mnthupi mwako tawugwire mtima Koma ngati sukwanitsa iwe udzigwiritsa ndati usaleke maloto ife mbuyomo ndi ako Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire? Ndani wina, tell me ndani wina Ndani wina tidzadalire?