Kishore Kumar Hits

Ritaa - Wa Ine текст песни

Исполнитель: Ritaa

альбом: Wa Ine

Внимание! Перевод текстов выполнен автоматически. Возможны неточности и неполнота перевода. Мы прилагаем все усилия для обеспечения точности перевода, но рекомендуем использовать его только в качестве общего ориентира.

Hmmm LeslieLeslie HmmmYea yea yeah, RitaaYea yea yeah, RitaaKodi ndi ndani?Kodi ndi ndani?Ukuimba foni ukufuna chani?Foni Ukuimba ukufuna chani?Ukuti ndimusiyeUkuti ndimusiyeUkukamba zosathekaUkukamba zosathekaZoti undiopseza zokhazo sizithekaZoti undiopseza zokhazo sizithekaIweyo ndi ndani?Iweyo ndi ndani?Umamuimbira foni ngati ndani?Foni Umamuimbira ngati ndani?Ukuzitaitsa nthawiNthawi UkuzitaitsaKunyumba kwanga nkomwe iye aliIye ali Kunyumba kwanga nkomweAmakonda tachitsikanaAmakonda tachitsikanaAnzako anandiuzaAnzako anandiuzaNdimampatsa zomwe amafunaNdimampatsa zomwe amafunaNdine amene amafunaNdine amene amafunaNdimampatsa zomwe amafunaNdimampatsa zomwe amafunaNdine amene amafunaNdine amene amafunaUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waAkamabisa foniAkamabisa foniSudabwa iwe eh eh?Sudabwa iwe eh eh?AdzakusiyaAdzakusiyaAkadzangotopa nawe eh ehAkadzangotopa nawe eh ehPhokoso la ChuleLa Chule PhokosoSililetsa ng'ombe kumwa madziNgombe Sililetsa kumwa madziLero ali ndi iwe, Mawa ali ndi ineLero ndi iwe ali, ali ndi ine MawaNdi m'mene zinthu zikhalireMmene Ndi zikhalire zinthuAmakonda mkazi wangwiroMkazi Amakonda wangwiroAnzako anakunamizaAnzako anakunamizaNdimampatsa zomwe amafunaNdimampatsa zomwe amafunaKukutaitsa Nthawi nzomwe akufunaNthawi Kukutaitsa nzomwe akufunaNdimampatsa zomwe amafunaNdimampatsa zomwe amafunaKukutaitsa Nthawi nzomwe akufunaNthawi Kukutaitsa nzomwe akufunaUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waNdithana nawe, nawe, musiyeNdithana nawe, nawe, musiyeNdithana nawe, nawe, ndisiyeNdithana nawe, nawe, ndisiyeUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine waUyu ndi wa ine, wa ine, wa ineIne ndi Uyu wa, wa ine, ine wa

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители

Piksy

Исполнитель

Dali

Исполнитель