Kishore Kumar Hits

Zonke Too Fresh - Amtenga текст песни

Исполнитель: Zonke Too Fresh

альбом: Amtenga


Man wo nda bhobho

Si andewu ngati achina thompo
Amatchilaso mwa bhobho
Komano mkaziyoo
Mkaziyo ndi wangwilo
Amafunika superhero
Komano man wo akumabwera ndi yawo yawo
Komano amtenga aah
Inuyo mupenga aa
Komano antenga aah
Inuyo mupeeee (nga)
Komano amtenga
Winayo watenga
Inuyo mupenga
Winayo wa nteee ee (nga)
Mkaziyo ndi wa bhobho
Komano man wooo
Alibe khalidwe
Mkazi amangomenya
Daily kugona ndi nkhawa
Kenako mudanda akathawa
Koma pena pake kumavomeleza
Onani bondo mwa nong'oneza
Yeeah
Lalalalalalala amutenga ena
Lalalalalalalala amutenga ena
Man wo nda bhobho
Si andewu ngati achina thompo
Amatchilaso mwa bhobho
Komano mkaziyoo
Mkaziyo ndi wangwilo
Amafunika superhero
Komano man wo akumabwera ndi yawo yawo
Komano amtenga aah
Inuyo mupenga aa
Komano antenga aah
Inuyo mupeeee (nga)

Iii inu ma man
Iii inu tamvani
Iii inu pali nkhani
Kwavuta Kumutsiku
Akuchita kungananana
Malaya kukwenyanana
Koma amavanana (nana)
Iyeeeeeh
Kulipo kuona ngati amakukonda
Komano utazisandusa wekha mlonda
Care for your partner suzapitaso kwa wina aah
Man wo nda bhobho
Si andewu ngati achina thompo
Amatchilaso mwa bhobho
Komano mkaziyoo
Mkaziyo ndi wangwilo
Amafunika superhero
Komano man wo akumabwera ndi yawo yawo
Komano amtenga aah
Inuyo mupenga aa
Komano antenga aah
Inuyo mupeeee (nga)

Care for your partner
Care for your partner
Care for your partner aaaah
Ayye Maone Awosh

Поcмотреть все песни артиста

Другие альбомы исполнителя

Похожие исполнители